-
2 Mafumu 14:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Koma ana a anthu omwe anapha bambo akewo sanawaphe, mogwirizana ndi lamulo la Yehova lomwe linalembedwa mʼChilamulo cha Mose lakuti: “Abambo asamaphedwe chifukwa cha zimene ana awo achita ndipo ana asamaphedwe chifukwa cha zimene abambo awo achita. Munthu aliyense aziphedwa chifukwa cha tchimo lake.”+
-