2 Mafumu 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Amaziya anatumiza anthu kwa Yehoasi mwana wa Yehoahazi mwana wa Yehu mfumu ya Isiraeli, kukamuuza kuti: “Bwera tidzamenyane.”+
8 Kenako Amaziya anatumiza anthu kwa Yehoasi mwana wa Yehoahazi mwana wa Yehu mfumu ya Isiraeli, kukamuuza kuti: “Bwera tidzamenyane.”+