2 Mafumu 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma Amaziya sanamvere.+ Choncho Yehoasi, mfumu ya Isiraeli, anapitadi ndipo iye ndi Amaziya mfumu ya Yuda anakumana nʼkuyamba kumenyana ku Beti-semesi+ mʼdziko la Yuda.+
11 Koma Amaziya sanamvere.+ Choncho Yehoasi, mfumu ya Isiraeli, anapitadi ndipo iye ndi Amaziya mfumu ya Yuda anakumana nʼkuyamba kumenyana ku Beti-semesi+ mʼdziko la Yuda.+