-
2 Mafumu 14:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Yehoasi anatenga golide ndi siliva yense komanso ziwiya zonse zimene anazipeza panyumba ya Yehova ndi mʼnyumba yosungiramo chuma cha mfumu. Anagwiranso anthu ena ndipo kenako anabwerera ku Samariya.
-