2 Mafumu 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Patapita nthawi, anthu ena anamukonzera chiwembu+ ku Yerusalemu, choncho iye anathawira ku Lakisi. Koma anthuwo anatumiza anthu ena omwe anamutsatira ku Lakisiko nʼkukamuphera komweko.
19 Patapita nthawi, anthu ena anamukonzera chiwembu+ ku Yerusalemu, choncho iye anathawira ku Lakisi. Koma anthuwo anatumiza anthu ena omwe anamutsatira ku Lakisiko nʼkukamuphera komweko.