2 Mafumu 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma Yehova analonjeza kuti sadzachotseratu dzina la Isiraeli padziko lapansi,+ choncho anawapulumutsa ndi dzanja la Yerobowamu mwana wa Yehoasi.+
27 Koma Yehova analonjeza kuti sadzachotseratu dzina la Isiraeli padziko lapansi,+ choncho anawapulumutsa ndi dzanja la Yerobowamu mwana wa Yehoasi.+