2 Mafumu 14:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Nkhani zina zokhudza Yerobowamu, zonse zimene anachita, mphamvu zake, mmene anamenyera nkhondo komanso mmene anabwezeretsera Damasiko+ ndi Hamati+ ku Yuda mu Isiraeli, zinalembedwa mʼbuku la mbiri ya mafumu a Isiraeli.
28 Nkhani zina zokhudza Yerobowamu, zonse zimene anachita, mphamvu zake, mmene anamenyera nkhondo komanso mmene anabwezeretsera Damasiko+ ndi Hamati+ ku Yuda mu Isiraeli, zinalembedwa mʼbuku la mbiri ya mafumu a Isiraeli.