-
2 Mafumu 15:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Azariya anakhala mfumu ali ndi zaka 16 ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 52. Amayi ake anali a ku Yerusalemu ndipo dzina lawo linali Yekoliya.
-