2 Mafumu 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komabe sanachotse malo okwezeka.+ Anthu ankaperekabe nsembe zautsi ndi nsembe zina mʼmalo okwezekawo.+
4 Komabe sanachotse malo okwezeka.+ Anthu ankaperekabe nsembe zautsi ndi nsembe zina mʼmalo okwezekawo.+