2 Mafumu 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako Azariya, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda a makolo ake+ mu Mzinda wa Davide. Ndiyeno Yotamu mwana wake anakhala mfumu mʼmalo mwake.
7 Kenako Azariya, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda a makolo ake+ mu Mzinda wa Davide. Ndiyeno Yotamu mwana wake anakhala mfumu mʼmalo mwake.