-
2 Mafumu 15:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Pa nthawi imeneyi mʼpamene Menahemu anachoka ku Tiriza nʼkupita kukaukira mzinda wa Tifisa. Iye anapha anthu onse amumzindawo ndiponso a mʼdera lozungulira chifukwa choti sanamutsegulire geti. Komanso anatumbula akazi onse oyembekezera.
-