2 Mafumu 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Menahemu anapeza ndalama zasilivazo kuchokera kwa Aisiraeli. Iye anasonkhetsa masekeli* 50 a siliva kwa mwamuna aliyense wachuma+ ndipo anawapereka kwa mfumu ya Asuri. Kenako mfumu ya Asuri inabwerera ndipo sinakhale mʼdzikomo.
20 Menahemu anapeza ndalama zasilivazo kuchokera kwa Aisiraeli. Iye anasonkhetsa masekeli* 50 a siliva kwa mwamuna aliyense wachuma+ ndipo anawapereka kwa mfumu ya Asuri. Kenako mfumu ya Asuri inabwerera ndipo sinakhale mʼdzikomo.