2 Mafumu 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kenako Hoshiya+ mwana wa Ela anakonzera chiwembu Peka mwana wa Remaliya nʼkumupha. Atatero anakhala mfumu mʼmalo mwake mʼchaka cha 20 cha Yotamu+ mwana wa Uziya.
30 Kenako Hoshiya+ mwana wa Ela anakonzera chiwembu Peka mwana wa Remaliya nʼkumupha. Atatero anakhala mfumu mʼmalo mwake mʼchaka cha 20 cha Yotamu+ mwana wa Uziya.