2 Mafumu 15:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Komabe sanachotse malo okwezeka ndipo anthu ankaperekabe nsembe zautsi komanso nsembe zina mʼmalo okwezekawo.+ Iye ndi amene anamanga geti lakumtunda la nyumba ya Yehova.+
35 Komabe sanachotse malo okwezeka ndipo anthu ankaperekabe nsembe zautsi komanso nsembe zina mʼmalo okwezekawo.+ Iye ndi amene anamanga geti lakumtunda la nyumba ya Yehova.+