2 Mafumu 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ahazi+ mwana wa Yotamu mfumu ya Yuda anakhala mfumu mʼchaka cha 17 cha Peka mwana wa Remaliya.