2 Mafumu 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ahazi anayamba kulamulira ali ndi zaka 20 ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 16. Iye sanachite zoyenera pamaso pa Yehova Mulungu wake ngati mmene anachitira Davide kholo lake.+
2 Ahazi anayamba kulamulira ali ndi zaka 20 ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 16. Iye sanachite zoyenera pamaso pa Yehova Mulungu wake ngati mmene anachitira Davide kholo lake.+