2 Mafumu 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa nthawiyo, Rezini mfumu ya Siriya analanda mzinda wa Elati+ nʼkuubwezera kwa Aedomu. Kenako anathamangitsa Ayuda mumzinda wa Elati ndipo Aedomu anayamba kukhala mumzindawu moti adakali momwemo mpaka lero.
6 Pa nthawiyo, Rezini mfumu ya Siriya analanda mzinda wa Elati+ nʼkuubwezera kwa Aedomu. Kenako anathamangitsa Ayuda mumzinda wa Elati ndipo Aedomu anayamba kukhala mumzindawu moti adakali momwemo mpaka lero.