2 Mafumu 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Ahazi anatenga siliva ndi golide wapanyumba ya Yehova ndiponso wochokera mʼnyumba ya mfumu nʼkutumiza kwa mfumu ya Asuri ngati chiphuphu.+
8 Kenako Ahazi anatenga siliva ndi golide wapanyumba ya Yehova ndiponso wochokera mʼnyumba ya mfumu nʼkutumiza kwa mfumu ya Asuri ngati chiphuphu.+