2 Mafumu 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Mfumu Ahazi anapita kukakumana ndi Tigilati-pilesere mfumu ya Asuri ku Damasiko. Kumeneko anaonako guwa lansembe, choncho Mfumu Ahazi anatumizira wansembe Uliya pulani ya guwalo.+
10 Kenako Mfumu Ahazi anapita kukakumana ndi Tigilati-pilesere mfumu ya Asuri ku Damasiko. Kumeneko anaonako guwa lansembe, choncho Mfumu Ahazi anatumizira wansembe Uliya pulani ya guwalo.+