2 Mafumu 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Wansembe Uliya+ anamanga guwalo+ mogwirizana ndi malangizo onse amene Mfumu Ahazi anamutumizira ali ku Damasiko. Wansembe Uliya anamaliza kumanga guwalo Mfumu Ahazi asanabwere kuchokera ku Damasiko.
11 Wansembe Uliya+ anamanga guwalo+ mogwirizana ndi malangizo onse amene Mfumu Ahazi anamutumizira ali ku Damasiko. Wansembe Uliya anamaliza kumanga guwalo Mfumu Ahazi asanabwere kuchokera ku Damasiko.