2 Mafumu 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mfumuyo itabwerako ku Damasiko, nʼkuona guwa lansembelo, inapita kukaperekapo nsembe.+