-
2 Mafumu 16:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Paguwapo, mfumuyo inapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zambewu. Inathiraponso nsembe zachakumwa ndiponso kuwazapo magazi a nsembe zake zamgwirizano.
-