-
2 Mafumu 16:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Mfumuyo inachotsa chinthu chokhala ndi denga chogwiritsa ntchito pa Sabata chimene anachimanga mʼnyumba ya Yehova ndipo inatsekanso khomo lakunja limene mfumu inkalowera mʼnyumbayo. Inachita zimenezi chifukwa cha mfumu ya Asuri.
-