2 Mafumu 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mʼchaka cha 12 cha Ahazi mfumu ya Yuda, Hoshiya+ mwana wa Ela anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya ndipo analamulira zaka 9.
17 Mʼchaka cha 12 cha Ahazi mfumu ya Yuda, Hoshiya+ mwana wa Ela anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya ndipo analamulira zaka 9.