2 Mafumu 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zimenezi zinachitika chifukwa chakuti Aisiraeli anachimwira Yehova Mulungu wawo, yemwe anawatulutsa mʼdziko la Iguputo nʼkuwachotsa mʼmanja mwa Farao mfumu ya Iguputo+ ndipo anayamba kulambira* milungu ina.+
7 Zimenezi zinachitika chifukwa chakuti Aisiraeli anachimwira Yehova Mulungu wawo, yemwe anawatulutsa mʼdziko la Iguputo nʼkuwachotsa mʼmanja mwa Farao mfumu ya Iguputo+ ndipo anayamba kulambira* milungu ina.+