-
2 Mafumu 17:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Iwo ankatsatira miyambo ya mitundu imene Yehova anaithamangitsa pamaso pa Aisiraeli ndiponso ankatsatira miyambo imene mafumu a Isiraeli anayambitsa.
-