2 Mafumu 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aisiraeli ankachita zinthu zosayenera kwa Yehova Mulungu wawo. Anapitiriza kumanga malo okwezeka mʼmizinda yawo yonse,+ kuyambira kunsanja ya alonda mpaka kumzinda wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri.*
9 Aisiraeli ankachita zinthu zosayenera kwa Yehova Mulungu wawo. Anapitiriza kumanga malo okwezeka mʼmizinda yawo yonse,+ kuyambira kunsanja ya alonda mpaka kumzinda wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri.*