2 Mafumu 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo anapitiriza kupereka nsembe zautsi pamalo okwezeka onse ngati mmene inkachitira mitundu imene Yehova anaithamangitsa mʼdzikolo chifukwa cha Aisiraeliwo.+ Iwo anapitiriza kuchita zinthu zoipa zokwiyitsa Yehova.
11 Iwo anapitiriza kupereka nsembe zautsi pamalo okwezeka onse ngati mmene inkachitira mitundu imene Yehova anaithamangitsa mʼdzikolo chifukwa cha Aisiraeliwo.+ Iwo anapitiriza kuchita zinthu zoipa zokwiyitsa Yehova.