2 Mafumu 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anapitiriza kulambira mafano onyansa*+ omwe Yehova anawauza kuti: “Musachite zimenezi.”+