1 Mbiri 1:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ana amene Ketura+ mkazi wamngʼono* wa Abulahamu anabereka, anali Zimirani, Yokesani, Medani, Midiyani,+ Isibaki ndi Shuwa.+ Ana a Yokesani anali Sheba ndi Dedani.+
32 Ana amene Ketura+ mkazi wamngʼono* wa Abulahamu anabereka, anali Zimirani, Yokesani, Medani, Midiyani,+ Isibaki ndi Shuwa.+ Ana a Yokesani anali Sheba ndi Dedani.+