1 Mbiri 1:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Mafumu amene analamulira dziko la Edomu,+ Aisiraeli* asanayambe kulamulidwa ndi mfumu ina iliyonse,+ ndi awa: Bela mwana wa Beori. Dzina la mzinda wake linali Dinihaba.
43 Mafumu amene analamulira dziko la Edomu,+ Aisiraeli* asanayambe kulamulidwa ndi mfumu ina iliyonse,+ ndi awa: Bela mwana wa Beori. Dzina la mzinda wake linali Dinihaba.