1 Mbiri 1:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Bela atamwalira, Yobabi mwana wa Zera wa ku Bozira,+ anayamba kulamulira mʼmalo mwake.