-
1 Mbiri 1:46Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
46 Husamu atamwalira, Hadadi mwana wa Bedadi, amene anagonjetsa Amidiyani mʼdera la Mowabu, anayamba kulamulira mʼmalo mwake. Dzina la mzinda wake linali Aviti.
-