-
1 Mbiri 1:50Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
50 Baala-hanani atamwalira, Hadadi anayamba kulamulira mʼmalo mwake. Dzina la mzinda wake linali Pau ndipo mkazi wake dzina lake linali Mehetabele mwana wamkazi wa Matiredi, mwana wamkazi wa Mezahabu.
-