1 Mbiri 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Abigayeli anabereka Amasa+ ndipo bambo ake a Amasa anali Yeteri mbadwa ya Isimaeli.