1 Mbiri 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako Gesuri+ ndi Siriya+ analanda Havoti-yairi.+ Analandanso Kenati+ ndi midzi yake yozungulira, mizinda 60. Onsewa anali ana a Makiri, bambo a Giliyadi.
23 Kenako Gesuri+ ndi Siriya+ analanda Havoti-yairi.+ Analandanso Kenati+ ndi midzi yake yozungulira, mizinda 60. Onsewa anali ana a Makiri, bambo a Giliyadi.