1 Mbiri 2:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ana a Kalebe,*+ mchimwene wake wa Yerameeli, anali Mesa mwana wake woyamba, yemwe anali bambo ake a Zifi. Panalinso ana a Maresha bambo ake a Heburoni.
42 Ana a Kalebe,*+ mchimwene wake wa Yerameeli, anali Mesa mwana wake woyamba, yemwe anali bambo ake a Zifi. Panalinso ana a Maresha bambo ake a Heburoni.