1 Mbiri 2:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Mabanja a alembi amene ankakhala ku Yabezi anali Atirati, Asimeati ndi Asukati. Amenewa anali Akeni+ amene anachokera kwa Hamati bambo a nyumba ya Rekabu.+
55 Mabanja a alembi amene ankakhala ku Yabezi anali Atirati, Asimeati ndi Asukati. Amenewa anali Akeni+ amene anachokera kwa Hamati bambo a nyumba ya Rekabu.+