1 Mbiri 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ana amene Davide anabereka ku Heburoni+ anali awa: woyamba Aminoni,+ mayi ake anali Ahinowamu+ a ku Yezereeli, wachiwiri Danieli, mayi ake anali Abigayeli+ a ku Karimeli,
3 Ana amene Davide anabereka ku Heburoni+ anali awa: woyamba Aminoni,+ mayi ake anali Ahinowamu+ a ku Yezereeli, wachiwiri Danieli, mayi ake anali Abigayeli+ a ku Karimeli,