1 Mbiri 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Onsewa anali ana a Davide, kuwonjezera pa ana amene akazi ake aangʼono* anamuberekera ndipo Tamara+ anali mchemwali wawo.
9 Onsewa anali ana a Davide, kuwonjezera pa ana amene akazi ake aangʼono* anamuberekera ndipo Tamara+ anali mchemwali wawo.