1 Mbiri 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Penueli anali bambo a Gedori ndipo Ezeri anali bambo a Husa. Amenewa anali ana a Hura,+ mwana woyamba wa Efurata ndiponso bambo a Betelehemu.+
4 Penueli anali bambo a Gedori ndipo Ezeri anali bambo a Husa. Amenewa anali ana a Hura,+ mwana woyamba wa Efurata ndiponso bambo a Betelehemu.+