1 Mbiri 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ashari,+ bambo a Tekowa,+ anali ndi akazi awiri, Hela ndi Naara.