-
1 Mbiri 4:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Amenewa anali ana a Bitiya, mwana wamkazi wa Farao, amene Meredi anamʼkwatira. (Mkazi wake wa Chiyuda anabereka Yeredi bambo a Gedori, Hiberi bambo a Soko ndi Yekutieli bambo a Zanowa.)
-