1 Mbiri 4:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Anthu ena a fuko la Simiyoni, amuna okwana 500, anapita kuphiri la Seiri+ ndipo amene ankawatsogolera anali Pelatiya, Neariya, Refaya ndi Uziyeli, ana a Isi.
42 Anthu ena a fuko la Simiyoni, amuna okwana 500, anapita kuphiri la Seiri+ ndipo amene ankawatsogolera anali Pelatiya, Neariya, Refaya ndi Uziyeli, ana a Isi.