1 Mbiri 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ngakhale kuti Yuda+ anali wamphamvu pakati pa azichimwene ake ndiponso kubanja lake kunachokera wodzakhala mtsogoleri,+ udindo wa woyamba kubadwa unali wa Yosefe. 1 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:2 Nsanja ya Olonda,10/1/2005, tsa. 9
2 Ngakhale kuti Yuda+ anali wamphamvu pakati pa azichimwene ake ndiponso kubanja lake kunachokera wodzakhala mtsogoleri,+ udindo wa woyamba kubadwa unali wa Yosefe.