1 Mbiri 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Baala anabereka Beeraha yemwe Tigilati-pilenesere,+ mfumu ya Asuri, anamutenga kupita naye ku ukapolo. Iye anali mtsogoleri wa anthu a fuko la Rubeni.
6 Baala anabereka Beeraha yemwe Tigilati-pilenesere,+ mfumu ya Asuri, anamutenga kupita naye ku ukapolo. Iye anali mtsogoleri wa anthu a fuko la Rubeni.