-
1 Mbiri 5:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Anthu a fuko la Rubeni, la Gadi ndi hafu ya fuko la Manase anali ndi asilikali amphamvu 44,760 onyamula zishango, malupanga, mauta komanso ophunzitsidwa bwino nkhondo.
-