1 Mbiri 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pa nkhondoyo, Mulungu anawathandiza moti mbadwa za Hagara ndi onse amene anali nawo anaperekedwa mʼmanja mwawo popeza anapempha Mulunguyo kuti awathandize ndipo iye anamva kupembedzera kwawo chifukwa anamʼkhulupirira.+ 1 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:20 Nsanja ya Olonda,10/1/2005, tsa. 9
20 Pa nkhondoyo, Mulungu anawathandiza moti mbadwa za Hagara ndi onse amene anali nawo anaperekedwa mʼmanja mwawo popeza anapempha Mulunguyo kuti awathandize ndipo iye anamva kupembedzera kwawo chifukwa anamʼkhulupirira.+