1 Mbiri 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu ambiri anaphedwa chifukwa Mulungu woona ndi amene anamenya nkhondoyo.+ Iwo anapitiriza kukhala mʼmalo a anthuwo mpaka nthawi imene anatengedwa kupita ku ukapolo.+
22 Anthu ambiri anaphedwa chifukwa Mulungu woona ndi amene anamenya nkhondoyo.+ Iwo anapitiriza kukhala mʼmalo a anthuwo mpaka nthawi imene anatengedwa kupita ku ukapolo.+