-
1 Mbiri 5:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Atsogoleri a nyumba za makolo awo anali awa: Eferi, Isi, Elieli, Azirieli, Yeremiya, Hodaviya ndi Yahadieli. Onsewa anali atsogoleri a nyumba za makolo awo, asilikali amphamvu ndiponso anthu otchuka.
-